Salimo 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yehova andipatse mphoto chifukwa choti ndine wolungama,+Komanso chifukwa choti ndine wosalakwa pamaso pake.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+
24 Yehova andipatse mphoto chifukwa choti ndine wolungama,+Komanso chifukwa choti ndine wosalakwa pamaso pake.+
21 Chifukwa maso a Yehova amaona chilichonse chimene munthu akuchita,Ndipo iye amafufuza njira zake zonse.+