Salimo 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake. Salimo 55:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu. Miyambo 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Woipa amakodwa ndi zolakwa zake zomwe,Ndipo adzamangidwa ndi zingwe za tchimo lake lomwe.+
16 Mavuto amene akuwayambitsawo adzabwerera pamutu pake,+Zinthu zachiwawa zimene akuchita zidzagwera paliwombo pake.
23 Koma inu Mulungu, mudzatsitsira oipawo mʼdzenje lakuya.+ Anthu amene ali ndi mlandu wa magazi komanso achinyengowo, sadzakwanitsa kukhala ngakhale hafu ya moyo wawo.+ Koma ine ndidzakhulupirira inu.