8 Ndiye palinso Simeyi wa ku Bahurimu, mwana wa Gera wa fuko la Benjamini. Iyeyu anandilankhula mawu onyoza kwambiri+ tsiku limene ndinkapita ku Mahanaimu.+ Koma atabwera kudzakumana nane pa Yorodano, ndinamulumbirira pamaso pa Yehova kuti: ‘Sindidzakupha ndi lupanga.’+