1 Mafumu 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndiponso maluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse.
18 Pamatabwa a mkungudza a mkati mwa nyumbayo anajambulapo mochita kugoba zokongoletsera zooneka ngati zipanda+ ndiponso maluwa.+ Mkati monse munali matabwa a mkungudza ndipo simunkaoneka mwala uliwonse.