-
Deuteronomo 28:21, 22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehova adzachititsa kuti matenda akukakamireni mpaka atakufafanizani mʼdziko limene mukupita kukalitenga kuti likhale lanu.+ 22 Yehova adzakulangani ndi chifuwa chachikulu, kutentha kwa thupi koopsa,+ kutupa, nyengo yotentha,* lupanga,+ mphepo yotentha yowononga mbewu ndi matenda a mbewu.+ Zimenezi zidzakuvutitsani mpaka mutatheratu.
-