Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ine ndinayamba kupembedzera Yehova nʼkunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu. Anthuwa ndi anu,*+ amene munawawombola ndi mphamvu yanu ndipo munawatulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu.+
5 Tsopano mukadzamvera mawu anga mosamala ndi kusunga pangano langa, mudzakhaladi chuma changa chapadera pa anthu onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
26 Ine ndinayamba kupembedzera Yehova nʼkunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu. Anthuwa ndi anu,*+ amene munawawombola ndi mphamvu yanu ndipo munawatulutsa mu Iguputo ndi dzanja lamphamvu.+