1 Mafumu 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka. 2 Mbiri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ufumu wa Rehobowamu utangokhazikika+ ndiponso iye atangokhala wamphamvu, iye ndi Aisiraeli onse anasiya Chilamulo cha Yehova.+
7 Pa nthawiyi mʼpamene Solomo anamangira Kemosi malo okwezeka.+ Kemosi anali mulungu wonyansa wa Amowabu ndipo anamʼmangira malowo paphiri lomwe linali pafupi ndi Yerusalemu. Anamangiranso Moleki,+ mulungu wonyansa wa Aamoni,+ malo okwezeka.
12 Ufumu wa Rehobowamu utangokhazikika+ ndiponso iye atangokhala wamphamvu, iye ndi Aisiraeli onse anasiya Chilamulo cha Yehova.+