Deuteronomo 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho anthu inu munayandikira nʼkuimirira mʼmunsi mwa phiri. Phirilo linkayaka moto umene unkafika kumwamba,* ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+
11 Choncho anthu inu munayandikira nʼkuimirira mʼmunsi mwa phiri. Phirilo linkayaka moto umene unkafika kumwamba,* ndipo kunali mdima ndi mtambo wakuda.+