18 Inu simunafike paphiri limene mungathe kulikhudza,+ loyaka moto,+ lokhala ndi mtambo wakuda, mdima wandiweyani, lowombedwa ndi mphepo yamkuntho+ 19 komanso limene panamveka kulira kwa lipenga+ ndi mawu a winawake+ ndipo anthu atawamva, anapempha kuti asawauzenso mawu ena.+