32 Kuwonjezera pamenepo, anamanga guwa lansembe la Baala mʼkachisi wa Baala+ amene iye anamanga ku Samariya. 33 Ahabu anaimikanso mzati wopatulika.+ Iye anachita zinthu zambiri zokwiyitsa Yehova Mulungu wa Isiraeli kuposa mafumu onse a Isiraeli amene anakhalapo iye asanakhale mfumu.