26 Choncho, Mulungu wa Isiraeli anachititsa Puli mfumu ya Asuri,+ (ameneyu anali Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri) kuti atenge anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase nʼkupita nawo ku Hala, ku Habori, ku Hara ndi kumtsinje wa Gozani+ ndipo akukhalabe kumeneko mpaka lero.