2 Mafumu 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+ 2 Mafumu 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Mʼmasiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri anabwera nʼkulanda Iyoni, Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori, Giliyadi+ ndi Galileya, dera lonse la Nafitali.+ Anatenga anthu akumeneku nʼkupita nawo ku Asuri.+
19 Puli+ mfumu ya Asuri anabwera mʼdzikomo ndipo Menahemu anamupatsa matalente* 1,000 a siliva chifukwa choti anamuthandiza kulimbitsa ufumu.+
29 Mʼmasiku a Peka mfumu ya Isiraeli, Tigilati-pilesere+ mfumu ya Asuri anabwera nʼkulanda Iyoni, Abele-beti-maaka,+ Yanoa, Kedesi,+ Hazori, Giliyadi+ ndi Galileya, dera lonse la Nafitali.+ Anatenga anthu akumeneku nʼkupita nawo ku Asuri.+