2 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mʼchaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu. 2 Mbiri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+ Yesaya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+ Hoseya 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli. Mateyu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Uziya anabereka Yotamu.+Yotamu anabereka Ahazi.+Ahazi anabereka Hezekiya.+
18 Mʼchaka chachitatu cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Hezekiya+ mwana wa Ahazi,+ mfumu ya Yuda anakhala mfumu.
29 Hezekiya+ anakhala mfumu ali ndi zaka 25 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake dzina lawo linali Abiya mwana wa Zekariya.+
1 Masomphenya amene Yesaya*+ mwana wa Amozi anaona, okhudza Yuda ndi Yerusalemu mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya,+ mafumu a Yuda:+
1 Yehova analankhula ndi Hoseya* mwana wa Beeri mʼmasiku a Uziya,+ Yotamu,+ Ahazi+ ndi Hezekiya+ mafumu a Yuda,+ ndiponso mʼmasiku a Yerobowamu+ mwana wa Yowasi+ mfumu ya Isiraeli.