Hoseya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa wagalukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa.Ndipo akazi awo apakati adzatumbulidwa.” Amosi 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,‘Mdani adzazungulira dziko lonse,+Ameneyo adzakufoola,Ndipo adzatenga zinthu munsanja zako zolimba.’+ Mika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja,Malo oyenera kudzalapo mpesa.Miyala yake ndidzaiponya* mʼchigwa.Ndipo maziko ake ndidzawafukula nʼkuwasiya pamtunda.
16 Samariya adzaimbidwa mlandu+ chifukwa wagalukira Mulungu wake.+ Iwo adzagwetsedwa ndi lupanga.+Ana awo adzaphwanyidwaphwanyidwa.Ndipo akazi awo apakati adzatumbulidwa.”
11 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,‘Mdani adzazungulira dziko lonse,+Ameneyo adzakufoola,Ndipo adzatenga zinthu munsanja zako zolimba.’+
6 Samariya ndidzamusandutsa bwinja,Malo oyenera kudzalapo mpesa.Miyala yake ndidzaiponya* mʼchigwa.Ndipo maziko ake ndidzawafukula nʼkuwasiya pamtunda.