Deuteronomo 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Musamalambire Yehova Mulungu wanu mwa njira imeneyi, chifukwa iwo amachitira milungu yawo zinthu zonse zonyansa zimene Yehova amadana nazo. Iwo amafika ngakhale powotcha ana awo aamuna ndi aakazi pamoto kuti ikhale nsembe kwa milungu yawo.+ 2 Mbiri 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+ 2 Mbiri 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli. Salimo 106:37, 38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ankapereka nsembe ana awo aamunaKomanso ana awo aakazi kwa ziwanda.+ 38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.
31 Musamalambire Yehova Mulungu wanu mwa njira imeneyi, chifukwa iwo amachitira milungu yawo zinthu zonse zonyansa zimene Yehova amadana nazo. Iwo amafika ngakhale powotcha ana awo aamuna ndi aakazi pamoto kuti ikhale nsembe kwa milungu yawo.+
28 Ahazi+ anakhala mfumu ali ndi zaka 20 ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 16. Iye sanachite zoyenera pamaso pa Yehova ngati mmene anachitira Davide kholo lake.+
3 Kuwonjezera pamenepo, Ahazi anapereka nsembe yautsi mʼChigwa cha Mwana wa Hinomu.* Iye anawotcha ana ake pamoto+ potsatira zinthu zonyansa zimene ankachita anthu a mitundu ina+ amene Yehova anawathamangitsa pamaso pa Aisiraeli.
37 Ankapereka nsembe ana awo aamunaKomanso ana awo aakazi kwa ziwanda.+ 38 Ankakhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna komanso a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.