-
Yoswa 21:32, 33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kuchokera mʼfuko la Nafitali, anawapatsa mzinda wothawirako+ munthu amene wapha mnzake, wa Kedesi+ ku Galileya ndi malo ake odyetserako ziweto. Anawapatsanso Hamoti-dori ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Karitani ndi malo ake odyetserako ziweto. Yonse inalipo mizinda itatu.
33 Mizinda yonse ya Agerisoni motsatira mabanja awo inalipo 13 ndi malo ake odyetserako ziweto.
-