50 Uike Alevi kuti aziyangʼanira chihema cha Umboni+ ndi ziwiya zake zonse komanso chilichonse cha mmenemo.+ Iwowo ndi amene azinyamula chihemacho ndi ziwiya zake zonse.+ Ndi amenenso azitumikira pachihemapo+ ndipo azimanga misasa yawo mozungulira chihemacho.+