1 Mbiri 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Davide atangoyamba kukhala mʼnyumba* yake, anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la pangano la Yehova likukhala mutenti.”+
17 Davide atangoyamba kukhala mʼnyumba* yake, anauza Natani+ mneneri kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene likasa la pangano la Yehova likukhala mutenti.”+