-
2 Mbiri 5:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Pamene anthu oimba malipenga ndi oimba pakamwa ankaimba mogwirizana potamanda ndi kuthokoza Yehova, pamene mawu a malipenga, zinganga ndi zoimbira zina ankamveka, komanso pamene ankatamanda Yehova ndi mawu akuti, “chifukwa iye ndi wabwino, chikondi chake chokhulupirika chidzakhalapo mpaka kalekale,”+ mtambo unadzaza nyumbayo, nyumba ya Yehova.+
-