17 Inu Mulungu wanga, ine ndikudziwa bwino kuti mumafufuza mitima+ ndiponso kuti mumakonda anthu okhulupirika.+ Ineyo ndapereka zinthu zonsezi mwakufuna kwanga komanso ndi mtima wopanda chinyengo. Ndasangalala kwambiri kuona anthu anu ali apawa, akupereka zopereka zawo mwakufuna kwawo.