Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la Pasika wa Yehova.+ Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+
5 Mʼmwezi woyamba, pa tsiku la 14 la mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la Pasika wa Yehova.+
16 “Muzikumbukira kuti mwezi wa Abibu* ndi wofunika ndipo muzichita chikondwerero cha Pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa mʼmwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+