-
2 Mbiri 32:7, 8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 “Limbani mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu. Musachite mantha kapena kuopa mfumu ya Asuri+ ndi gulu lalikulu limene ali nalo, chifukwa ife tili ndi ambiri kuposa amene ali ndi mfumuyo.+ 8 Iye akudalira mphamvu za anthu, koma ife tili ndi Yehova Mulungu wathu kuti atithandize ndi kutimenyera nkhondo zathu.”+ Anthuwo analimbikitsidwa kwambiri ndi mawu amene Hezekiya mfumu ya Yuda inanenawa.+
-