2 Samueli 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamalowo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliri umene unagwa mu Isiraeliwo, unatha. 1 Mbiri 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti apite kumalo opunthira mbewu a Orinani wa Chiyebusi, nʼkukamangira Yehova guwa lansembe.+
25 Zitatero, Davide anamangira Yehova guwa lansembe+ pamalowo ndipo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano. Choncho Yehova anamva kuchonderera kwawo,+ moti mliri umene unagwa mu Isiraeliwo, unatha.
18 Ndiyeno mngelo wa Yehova anauza Gadi+ kuti auze Davide kuti apite kumalo opunthira mbewu a Orinani wa Chiyebusi, nʼkukamangira Yehova guwa lansembe.+