-
2 Mafumu 18:15, 16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Choncho Hezekiya anapereka siliva yense amene anali panyumba ya Yehova ndiponso amene anali mosungira chuma cha mʼnyumba ya mfumu.+ 16 Pa nthawi imeneyi Hezekiya mfumu ya Yuda anachotsa zitseko za kachisi+ wa Yehova ndi mafelemu ake, zimene iye anazikuta ndi golide,+ nʼkupereka golideyo kwa mfumu ya Asuri.
-