Yeremiya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipotu kungoyambira nthawi imene tinasiya kupereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba,* tikusowa chilichonse ndipo tawonongeka ndi lupanga komanso njala.”
18 Ndipotu kungoyambira nthawi imene tinasiya kupereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba,* tikusowa chilichonse ndipo tawonongeka ndi lupanga komanso njala.”