-
1 Mafumu 14:22, 23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Ayuda ankachita zoipa pamaso pa Yehova+ ndipo anamukwiyitsa kwambiri ndi machimo awo kuposa mmene makolo awo anachitira.+ 23 Nawonso anapitiriza kumanga malo okwezeka, zipilala zopatulika ndi mizati yopatulika*+ pamwamba pa phiri lililonse lalitali+ ndiponso pansi pa mtengo uliwonse waukulu wamasamba obiriwira.+
-