22 Ndinachita manyazi kupempha asilikali kwa mfumu ndi okwera pamahatchi kuti atiteteze kwa adani mʼnjira, chifukwa tinali titauza mfumuyo kuti: “Dzanja labwino la Mulungu wathu limathandiza anthu onse omufunafuna,+ koma amasonyeza mkwiyo ndi mphamvu zake kwa onse omusiya.”+