Deuteronomo 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+ Yoswa 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukumenyerani nkhondo+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+
30 Yehova Mulungu wanu adzakutsogolerani ndipo adzakumenyerani nkhondo,+ ngati mmene anachitira ku Iguputo inu mukuona.+
10 Munthu mmodzi yekha wa inu adzathamangitsa anthu 1,000,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu akukumenyerani nkhondo+ mogwirizana ndi zimene anakulonjezani.+