Deuteronomo 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a mʼChilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’”)
26 ‘Wotembereredwa ndi munthu amene sadzatsatira mawu a mʼChilamulo ichi ndipo sadzawagwiritsa ntchito.’+ (Anthu onse azidzayankha kuti, ‘Zikhale momwemo!’”)