Ekisodo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu. Musamagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo amene akukhala mumzinda wanu.*+ Ekisodo 34:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Muzigwira ntchito zanu kwa masiku 6, koma pa tsiku la 7 muzipuma.*+ Ngakhale pa nthawi yolima ndi yokolola muzipuma. Ekisodo 35:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muzigwira ntchito masiku 6, koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+
10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu. Musamagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo amene akukhala mumzinda wanu.*+
21 Muzigwira ntchito zanu kwa masiku 6, koma pa tsiku la 7 muzipuma.*+ Ngakhale pa nthawi yolima ndi yokolola muzipuma.
2 Muzigwira ntchito masiku 6, koma tsiku la 7 likhale lopatulika kwa inu, likhale sabata la Yehova lopuma pa ntchito zanu zonse.+ Aliyense wogwira ntchito pa tsikuli adzaphedwa.+