Salimo 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako anthu adzati: “Ndithudi wolungama amalandira mphoto.+ Ndithudi pali Mulungu amene amaweruza padziko lapansi.”+ Mateyu 7:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Siyani kuweruza ena+ kuti inunso musaweruzidwe, Aroma 14:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa+ chifukwa Yehova* akhoza kumuthandiza kuti zimuyendere bwino. Yakobo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+
11 Kenako anthu adzati: “Ndithudi wolungama amalandira mphoto.+ Ndithudi pali Mulungu amene amaweruza padziko lapansi.”+
4 Ndiwe ndani kuti uweruze wantchito wa mnzako?+ Ndi udindo wa bwana wake kumuweruza kuti ndi wolakwa kapena wosalakwa+ chifukwa Yehova* akhoza kumuthandiza kuti zimuyendere bwino.
12 Komatu Wopereka Malamulo komanso Woweruza alipo mmodzi yekha,+ amenenso akhoza kupulumutsa ndi kuwononga.+ Ndiye iwe ndiwe ndani kuti uziweruza mnzako?+