10 Munthu asakunyozeni chifukwa chakuti munayamba kumanga ndi zinthu zochepa.+ Popeza anthu adzasangalala ndipo adzaona chingwe choyezera cha mmisiri womanga, mʼdzanja la Zerubabele. Nyale 7 zimenezi ndi maso a Yehova amene akuyangʼana uku ndi uku padziko lonse lapansi.”+