1 Timoteyo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usadzudzule mokalipa mwamuna wachikulire,+ koma uzilankhula naye mokoma mtima ngati bambo ako. Amuna achinyamata uzilankhula nawo ngati achimwene ako 1 Petulo 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+
5 Usadzudzule mokalipa mwamuna wachikulire,+ koma uzilankhula naye mokoma mtima ngati bambo ako. Amuna achinyamata uzilankhula nawo ngati achimwene ako
5 Chimodzimodzinso inu achinyamata, muzigonjera amuna achikulire.*+ Komanso nonsenu muzichitirana zinthu modzichepetsa* chifukwa Mulungu sasangalala ndi anthu odzikuza. Koma anthu odzichepetsa amawasonyeza kukoma mtima kwake kwakukulu.+