Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, simungaphe munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama alangidwe limodzi ndi woipa.+ Simungachite zimenezo.+ Ndinu Woweruza wa dziko lonse lapansi. Ndiye kodi simuchita chilungamo?”+ 2 Mbiri 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+ Salimo 92:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo adzalengeza kuti Yehova ndi wolungama. Iye ndi Thanthwe langa,+ ndipo sachita zosalungama.
25 Simungachite zimenezo, simungaphe munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama alangidwe limodzi ndi woipa.+ Simungachite zimenezo.+ Ndinu Woweruza wa dziko lonse lapansi. Ndiye kodi simuchita chilungamo?”+
7 Muziopa Yehova+ ndipo muzisamala pochita zinthu, chifukwa Yehova Mulungu wathu si wopanda chilungamo+ kapena watsankho,+ ndipo salandira chiphuphu.”+