Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+ Salimo 103:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Masiku a moyo wa munthu ali ngati masiku a udzu.+Iye amaphuka ngati duwa lakutchire.+ Salimo 144:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Yehova, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira?Kodi mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimuwerengera?+
4 Ndimaganiza kuti, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira,Ndipo mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimusamalira?+
3 Inu Yehova, munthu ndi ndani kuti muzimuganizira?Kodi mwana wa munthu ndi ndani kuti muzimuwerengera?+