Genesis 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Simungachite zimenezo, simungaphe munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama alangidwe limodzi ndi woipa.+ Simungachite zimenezo.+ Ndinu Woweruza wa dziko lonse lapansi. Ndiye kodi simuchita chilungamo?”+ Salimo 82:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyamukani inu Mulungu, ndipo muweruze dziko lapansi,+Chifukwa mitundu yonse ya anthu ndi yanu.
25 Simungachite zimenezo, simungaphe munthu wolungama limodzi ndi woipa. Sizingatheke kuti wolungama alangidwe limodzi ndi woipa.+ Simungachite zimenezo.+ Ndinu Woweruza wa dziko lonse lapansi. Ndiye kodi simuchita chilungamo?”+