Salimo 22:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+ Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”
27 Anthu onse ochokera kumalekezero a dziko lapansi adzakumbukira Yehova nʼkupita kwa iye. Ndipo mabanja onse a mitundu ya anthu adzagwada pamaso panu.+
4 Popeza inu nokha Yehova* ndinu wokhulupirika, ndi ndani amene sadzakuopani komanso kulemekeza dzina lanu?+ Anthu a mitundu yonse adzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa iwo adziwa malamulo anu olungama.”