Chivumbulutso 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:4 Yandikirani, ptsa. 282-283 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218 Nsanja ya Olonda,4/1/1996, ptsa. 14-151/1/1992, ptsa. 18-19
4 Kodi ndani sadzakuopani,+ inu Yehova?+ Ndani sadzalemekeza dzina lanu?+ Pakuti inu nokha ndinu wokhulupirika.+ Mitundu yonse ya anthu idzabwera kudzalambira pamaso panu,+ chifukwa malamulo anu olungama aonekera.”+
15:4 Yandikirani, ptsa. 282-283 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 217-218 Nsanja ya Olonda,4/1/1996, ptsa. 14-151/1/1992, ptsa. 18-19