-
Salimo 144:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Tambasulani manja anu kuchokera kumwamba.
Ndilanditseni ndi kundipulumutsa mʼmadzi amphamvu,
Ndilanditseni mʼmanja mwa anthu achilendo,+
-
Maliro 3:54Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
54 Ndinamira mʼmadzi moti ndinanena kuti: “Ndifa basi!”
-
-
Yona 2:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Zomera zamʼnyanja zinakulunga mutu wanga.
-
-
-