2 Samueli 22:17, 18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba;Anandigwira nʼkundivuula mʼmadzi akuya.+ 18 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Kwa anthu odana nane amene anali amphamvu kuposa ine. Salimo 18:16, 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba,Anandigwira nʼkundivuula mʼmadzi akuya.+ 17 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Kwa anthu odana nane amene anali amphamvu kuposa ine.+ Salimo 54:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa anthu achilendo andiukira,Ndipo anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga.+ Iwo salemekeza Mulungu.*+ (Selah)
17 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba;Anandigwira nʼkundivuula mʼmadzi akuya.+ 18 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Kwa anthu odana nane amene anali amphamvu kuposa ine.
16 Anatambasula dzanja lake kuchokera kumwamba,Anandigwira nʼkundivuula mʼmadzi akuya.+ 17 Anandipulumutsa kwa mdani wanga wamphamvu,+Kwa anthu odana nane amene anali amphamvu kuposa ine.+
3 Chifukwa anthu achilendo andiukira,Ndipo anthu ankhanza akufunafuna moyo wanga.+ Iwo salemekeza Mulungu.*+ (Selah)