2 Samueli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi mchimwene wake Bana, ana a Rimoni wa ku Beeroti kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, amene anandipulumutsa mʼmasautso anga onse,+ Salimo 103:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amawombola moyo wako kudzenje,*+Ndipo amakuveka chikondi chake chokhulupirika komanso chifundo ngati chisoti chachifumu.+
9 Koma Davide anayankha Rekabu ndi mchimwene wake Bana, ana a Rimoni wa ku Beeroti kuti: “Ndikulumbira mʼdzina la Yehova Mulungu wamoyo, amene anandipulumutsa mʼmasautso anga onse,+
4 Iye amawombola moyo wako kudzenje,*+Ndipo amakuveka chikondi chake chokhulupirika komanso chifundo ngati chisoti chachifumu.+