Genesis 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kudzera mwa mbadwa* yako,+ mitundu yonse yapadziko lapansi idzapeza madalitso chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+ Agalatiya 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Cholinga chake chinali chakuti kudzera mwa Khristu Yesu, mitundu ya anthu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.
18 Kudzera mwa mbadwa* yako,+ mitundu yonse yapadziko lapansi idzapeza madalitso chifukwa chakuti wamvera mawu anga.’”+
14 Cholinga chake chinali chakuti kudzera mwa Khristu Yesu, mitundu ya anthu ipeze madalitso amene Abulahamu analonjezedwa,+ kuti tidzalandire mzimu wolonjezedwawo+ chifukwa cha chikhulupiriro chathu.