Salimo 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”*
5 Yehova wanena kuti: “Chifukwa chakuti ovutika akuponderezedwaChifukwa cha kuusa moyo kwa anthu osauka,+Ndidzanyamuka nʼkuchitapo kanthu, Ndidzawapulumutsa kwa anthu amene akuwanyoza.”*