Salimo 104:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye wakhazikitsa dziko lapansi pamaziko ake.+Silidzasunthidwa pamalo ake* mpaka kalekale.+ Salimo 119:90 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwo yonse.+ Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lipitirizebe kukhalapo.+ Mlaliki 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mʼbadwo umapita ndipo mʼbadwo wina umabwera,Koma dziko lapansi lidzakhalapobe mpaka kalekale.+
90 Kukhulupirika kwanu kudzakhalapobe ku mibadwo yonse.+ Mwakhazikitsa mwamphamvu dziko lapansi, kuti lipitirizebe kukhalapo.+