Mika 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ine ndinati: “Tamverani inu atsogoleri a mbadwa za YakoboNdiponso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli.+ Kodi simukuyenera kudziwa chilungamo?
3 Ine ndinati: “Tamverani inu atsogoleri a mbadwa za YakoboNdiponso inu olamulira a nyumba ya Isiraeli.+ Kodi simukuyenera kudziwa chilungamo?