Amosi 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wanena kuti,‘Popeza Turo anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo,Ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pachibale.+
9 Yehova wanena kuti,‘Popeza Turo anandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.Chifukwa anapereka ku Edomu gulu lonse la anthu ogwidwa ukapolo,Ndiponso chifukwa chakuti sanakumbukire pangano la pachibale.+