Salimo 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+ Salimo 43:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+ Salimo 46:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pali mtsinje umene nthambi zake zimachititsa kuti anthu amumzinda wa Mulungu asangalale,+Chihema chachikulu chopatulika cha Wamʼmwambamwamba.
4 Ndapempha chinthu chimodzi kwa Yehova,Chimenecho ndi chimene ndikuchilakalaka.Chinthu chake nʼchakuti, ndikhale mʼnyumba ya Yehova masiku onse a moyo wanga,+Kuti ndione ubwino wa Yehova,Komanso kuti ndiyangʼane kachisi wake* moyamikira.*+
3 Tumizani kuwala kwanu ndi choonadi chanu.+ Zimenezi zinditsogolere.+Zinditsogolere kuphiri lanu lopatulika ndi kuchihema chanu chachikulu.+
4 Pali mtsinje umene nthambi zake zimachititsa kuti anthu amumzinda wa Mulungu asangalale,+Chihema chachikulu chopatulika cha Wamʼmwambamwamba.