1 Mbiri 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+ Salimo 78:68, 69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene amalikonda.+ 69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+
16 Choncho anabweretsa Likasa la Mulungu woona pamalo amene Davide anakonza nʼkuliika mutenti imene iye anamanga kuti lizikhalamo.+ Kenako iwo anapereka nsembe zopsereza ndi nsembe zamgwirizano kwa Mulungu woona.+
68 Koma anasankha fuko la Yuda,+Phiri la Ziyoni limene amalikonda.+ 69 Anachititsa kuti malo ake opatulika akhalepo mpaka kalekale ngati kumwamba,*+Ngati dziko lapansi limene analikhazikitsa mpaka kalekale.+