-
Yesaya 40:29-31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa
Ndipo munthu amene alibe mphamvu amamupatsa mphamvu zambiri.+
30 Anyamata adzatopa nʼkufooka,
Ndipo amuna achinyamata adzapunthwa nʼkugwa,
31 Koma anthu amene amayembekezera Yehova adzapezanso mphamvu.
Iwo adzaulukira mʼmwamba ngati kuti ali ndi mapiko a chiwombankhanga.+
Adzathamanga koma osafooka.
Adzayenda koma osatopa.”+
-