1 Mbiri 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ukadzamwalira nʼkugona mʼmanda ndi makolo ako, ndidzachititsa kuti mbadwa* yako, mmodzi wa ana ako,+ akhale mfumu ndipo ndidzachititsa kuti ufumu wake ukhazikike.+ Chivumbulutso 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+
11 Ukadzamwalira nʼkugona mʼmanda ndi makolo ako, ndidzachititsa kuti mbadwa* yako, mmodzi wa ana ako,+ akhale mfumu ndipo ndidzachititsa kuti ufumu wake ukhazikike.+
16 ‘Ine Yesu, ndinatumiza mngelo wanga kuti adzachitire umboni zinthu zimenezi kwa iwe kuti zithandize mipingo. Ine ndine muzu komanso mbadwa ya Davide.+ Ndinenso nthanda yowala kwambiri.’”+